Frobits
🎵 A song made on Frobits

Walk With Jesus

Mike Michaelz · 🇿🇲 Zambia
0:000:00
Download Remix
Make your own song
Continues securely on the web
Lyrics

*Verse 1*

Njira

yanga

sindidziwa,

'Tate

muikonza;

Komatu

ndizindikira

Kuti

mundikonda. *

Chorus*

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu *

Verse 2*

M'mene

mantha

andigwira,

Andidetsa

m'mtima,

Mbuye,

ndithawire

kwanu

Poti

mundikonda. *

Chorus*

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu *

Verse 3*

Sindidziwatu

zamawa,

Koma

sindiopa;

Ndidzakhulupira

Inu

Kuti

mundikonda. *

Chorus*

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu *

Verse 4*

Inde

wakukonda

ndinu;

Mawuwo

oona

Andidzaza

ndi

chimwemwe:

Mlungu

andikonda. *

Chorus (

Final)*

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu

Tiye.....

Tiye......

Tiyende

na

Yesu

Kakale

ena

safuna

kuyenda

na

Yesu

More songs by Mike Listen to songs created by others
FROBITS