[male vocals] Oyee,
onananana!
It's
a
boy,
Sky
Pizo,
mwana
wa
munyanja!
Aweh,
yebo,
let's
go!
Tivotele
Emmanuel
Mwanza,
WDC
wathu
muno
mu
community
Emmanuel
Mwanza,
munthu
wa
lusumpuko,
mavoti
yathu
tiyen
timupase
Makalanguzu
na
Kangongo,
timupase
mavoti
Emmanuel
Mwanza,
munthu
wa
lusumpuko
muno
mukasiya
Eish,
sharp
sharp!
Emmanuel
Mwanza,
mwana
wa
pakhomo!
Mavoti
yathu,
timupase
tonse!
Emmanuel
Mwanza,
mwana
wa
pakhomo!
Community
yathu,
ikhale
yatsopano!
Anthu
onse
apano
pa
dam,
tisegule
maso
Ngati
tifuna
lusumpuko,
Emmanuel
Mwanza
Munthu
wa
lusumpuko,
mavoti
yathu
tiyen
timupase
Pamene
tivota,
tisaone
pa
mutundu
Kapena
kuyangana
nkhope,
asambe!
Emmanuel
Mwanza
ni
mwana
wa
pakhomo,
voti
yanthu
timupase
Emmanuel
Mwanza,
mwana
wa
pakhomo!
Mavoti
yathu,
timupase
tonse!
Emmanuel
Mwanza,
mwana
wa
pakhomo!
Community
yathu,
ikhale
yatsopano!
Kumakalanguzu,
anthu
onse
avomela
Kuvotela
Emmanuel
Mwanza,
WDC
wa
anthu
Muno
munatebe
community,
anthu
onse
takonzeke
Kumuvotela
Emmanuel
Mwanza,
konse
ku
Kangongo
Avomela
Emmanuel
Mwanza
kuti
akhale
WDC!
Muno
mu
community
iyeee,
tidziwa
ndani!
Emmanuel
Mwanza,
mtsogoleri
wathu!
Tiyeni
tonse
pamodzi,
timupatse
mphamvu!
Mavoti
yathu
onse,
kwa
Emmanuel
Mwanza!
Emmanuel
Mwanza,
mwana
wa
pakhomo!
Mavoti
yathu,
timupase
tonse!
Emmanuel
Mwanza,
mwana
wa
pakhomo!
Community
yathu,
ikhale
yatsopano!
Emmanuel
Mwanza,
WDC
wathu!
Sho,
asambe,
let's
go!
Mwana
wa
pakhomo,
lusumpuko!
Emmanuel
Mwanza,
oyeee!